Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mika anali ndi nyumba ya milungu,+ chotero anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake mphamvu,*+ kuti azitumikira monga wansembe wake.+

  • 1 Samueli 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Amithengawo atalowa, anangopeza fano la terafi lili pabedi, ukonde waubweya wa mbuzi uli pamene Davide anali kutsamiritsa mutu wake.

  • Ezekieli 21:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mfumu ya Babulo yaima chilili pamene panakumana misewu iwiri kuti iwombeze maula.+ Mfumuyo yagwedeza mivi, yafunsira kwa aterafi*+ ndi kuyang’ana pachiwindi cha nyama.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena