Genesis 29:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehova ataona kuti Leya sanali kukondedwa kwenikweni, anam’patsa mphamvu zobereka,+ koma Rakele anali wosabereka.+ 1 Samueli 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndinali kupemphera kuti Yehova andipatse mwana uyu, kuti andipatse+ chimene ndinam’pempha.+ Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+
31 Yehova ataona kuti Leya sanali kukondedwa kwenikweni, anam’patsa mphamvu zobereka,+ koma Rakele anali wosabereka.+