Salimo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwaipatsa zokhumba za mtima wake,+Ndipo simunaimane zokhumba za pakamwa pake.+ [Seʹlah.] Salimo 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso sangalala mwa Yehova,+Ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako.+