Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsoka iwe Mowabu! Ndithu mudzafafanizika, inu anthu a Kemosi!+

      Ndithudi, iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzapereka ana ake aakazi mu ukapolo kwa Sihoni, mfumu ya Aamori.

  • Salimo 96:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+

      Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+

  • 1 Akorinto 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti ngakhale ilipo yotchedwa “milungu,”+ kaya kumwamba+ kapena padziko lapansi,+ ndipo n’zoona ilipodi “milungu” yambiri ndi “ambuye” ambiri,+

  • 2 Petulo 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mwambi woona uja wakwaniritsidwa pa iwo. Mwambiwo umati: “Galu+ wabwerera kumasanzi ake, ndipo nkhumba imene inasambitsidwa yapita kukagubudukanso m’matope.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena