Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Atatero iwo analiranso mokweza mawu. Kenako Olipa anapsompsona apongozi ake powatsanzika. Koma Rute anawaumirirabe.+

  • Rute 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno Rute anati: “Musandichonderere kuti ndikusiyeni, kuti ndibwerere ndisakutsatireni, pakuti kumene inu mupite inenso ndipita komweko, kumene inu mugone inenso ndigona komweko.+ Anthu a mtundu wanu adzakhala anthu a mtundu wanga,+ ndipo Mulungu wanu adzakhala Mulungu wanga.+

  • Rute 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano usachite mantha mwana wanga. Ndidzakuchitira zonse zimene wanena,+ chifukwa aliyense mumzinda wathu akudziwa kuti ndiwe mkazi wabwino kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena