Rute 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wakhala ukukunkha pambuyo pa atsikana antchito a Boazi. Kodi iye si wachibale wathu?+ Pajatu usiku walero akhala akupeta+ balere pamalo ake opunthira. Rute 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komano ngakhale kuti ndinedi wokuwombolani,+ pali wachibale wina wapafupi kwambiri kuposa ine+ amene angakuwombole.
2 Wakhala ukukunkha pambuyo pa atsikana antchito a Boazi. Kodi iye si wachibale wathu?+ Pajatu usiku walero akhala akupeta+ balere pamalo ake opunthira.
12 Komano ngakhale kuti ndinedi wokuwombolani,+ pali wachibale wina wapafupi kwambiri kuposa ine+ amene angakuwombole.