Rute 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maso ako akhale pamunda umene akukolola, ndipo uzipita nawo limodzi kumeneko. Anyamatawa ndawalamula kuti asakukhudze.+ Ukamva ludzu, nawenso uzipita kumitsuko kukamwa madzi amene anyamatawa azitunga.”+ 1 Timoteyo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo akazi achikulire+ ngati amayi ako. Akazi achitsikana uwadandaulire ngati alongo ako,+ ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse oipa.
9 Maso ako akhale pamunda umene akukolola, ndipo uzipita nawo limodzi kumeneko. Anyamatawa ndawalamula kuti asakukhudze.+ Ukamva ludzu, nawenso uzipita kumitsuko kukamwa madzi amene anyamatawa azitunga.”+
2 ndipo akazi achikulire+ ngati amayi ako. Akazi achitsikana uwadandaulire ngati alongo ako,+ ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse oipa.