Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 31:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pa nthawiyi n’kuti Labani atapita kukameta ubweya wa nkhosa zake. Akali kumeneko, Rakele anaba aterafi*+ a bambo ake.

  • Genesis 31:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ngati wachoka chifukwa cholakalaka kwambiri kunyumba kwa bambo ako, nanga n’chifukwa chiyani waba milungu yanga?”+

  • Oweruza 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mika anali ndi nyumba ya milungu,+ chotero anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake mphamvu,*+ kuti azitumikira monga wansembe wake.+

  • 1 Samueli 15:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti kupanduka+ n’chimodzimodzi ndi tchimo la kuwombeza,+ ndipo kuchita zinthu modzikuza n’chimodzimodzi ndi kugwiritsa ntchito mphamvu zamatsenga ndiponso aterafi.+ Popeza iwe wakana mawu a Yehova,+ iyenso wakukana kuti usakhalenso mfumu.”+

  • 2 Mafumu 23:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yosiya anachotsanso anthu olankhula ndi mizimu+ ndi olosera+ zam’tsogolo. Anachotsanso aterafi,*+ mafano onyansa,+ ndi zonyansa+ zonse zimene zinali m’dziko la Yuda ndi mu Yerusalemu, kuti atsatire mawu a chilamulo+ amene analembedwa m’buku+ limene wansembe Hilikiya analipeza panyumba ya Yehova.+

  • Hoseya 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa masiku ambiri, ana a Isiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe,+ chipilala chopatulika, efodi,+ ndi aterafi.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena