Miyambo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+ koma pakamwa pa zitsiru pamasefukira mawu opusa.+ Miyambo 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amene amadzikuza akapsa mtima, amatchedwa wodzikuza, wonyada ndi wodzitama.+ Aefeso 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kuwawidwa mtima konse kwa njiru,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata ndiponso mawu achipongwe+ zichotsedwe mwa inu limodzi ndi zoipa zonse.+
2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+ koma pakamwa pa zitsiru pamasefukira mawu opusa.+
31 Kuwawidwa mtima konse kwa njiru,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata ndiponso mawu achipongwe+ zichotsedwe mwa inu limodzi ndi zoipa zonse.+