1 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu. 2 Samueli 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide ankavina mozungulira pamaso pa Yehova ndi mphamvu zake zonse. Apa n’kuti Davide atavala efodi+ wansalu.
18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu.
14 Davide ankavina mozungulira pamaso pa Yehova ndi mphamvu zake zonse. Apa n’kuti Davide atavala efodi+ wansalu.