1 Samueli 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano imva izi, masiku adzafika pamene ndidzadula dzanja lako ndi la nyumba ya kholo lako, moti m’nyumba yako simudzakhala munthu wokalamba.+ 2 Mbiri 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamapeto pake anthuwo anam’konzera chiwembu+ ndipo anam’ponya miyala+ pabwalo la nyumba ya Yehova, atalamulidwa ndi mfumu. Miyambo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu okonda kukhetsa magazi amadana ndi aliyense wopanda cholakwa,+ koma anthu owongoka mtima amasamalira moyo wa anthu opanda cholakwawo.+
31 Tsopano imva izi, masiku adzafika pamene ndidzadula dzanja lako ndi la nyumba ya kholo lako, moti m’nyumba yako simudzakhala munthu wokalamba.+
21 Pamapeto pake anthuwo anam’konzera chiwembu+ ndipo anam’ponya miyala+ pabwalo la nyumba ya Yehova, atalamulidwa ndi mfumu.
10 Anthu okonda kukhetsa magazi amadana ndi aliyense wopanda cholakwa,+ koma anthu owongoka mtima amasamalira moyo wa anthu opanda cholakwawo.+