Salimo 56:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzadalira inu, tsiku lililonse limene ndingachite mantha.+