1 Samueli 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo wansembeyo anam’patsa mkate wopatulika,+ chifukwa panalibe mkate wina koma mkate wachionetsero wokha, umene anali atauchotsa pamaso pa Yehova+ pa tsiku limenelo kuti aikepo watsopano.
6 Pamenepo wansembeyo anam’patsa mkate wopatulika,+ chifukwa panalibe mkate wina koma mkate wachionetsero wokha, umene anali atauchotsa pamaso pa Yehova+ pa tsiku limenelo kuti aikepo watsopano.