1 Samueli 14:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pamenepo Sauli anati: “Mulungu andilange mowirikiza+ ngati suufa ndithu,+ Yonatani.” 1 Samueli 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Masiku onse amene mwana wa Jeseyo adzakhala ndi moyo, iweyo ndi ufumu wako sudzakhazikika ayi.+ Choncho tumiza anthu akamugwire ndi kumubweretsa kwa ine, pakuti ayenera kufa ndithu.”+ Miyambo 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu okonda kuchita zoipa sangamvetse chilungamo, koma amene akufunafuna Yehova amamvetsa chilichonse.+ Miyambo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtsogoleri woipa wolamulira anthu onyozeka ali ngati mkango wobangula ndiponso chimbalangondo chimene chikubwera kudzakuluma.+
31 Masiku onse amene mwana wa Jeseyo adzakhala ndi moyo, iweyo ndi ufumu wako sudzakhazikika ayi.+ Choncho tumiza anthu akamugwire ndi kumubweretsa kwa ine, pakuti ayenera kufa ndithu.”+
5 Anthu okonda kuchita zoipa sangamvetse chilungamo, koma amene akufunafuna Yehova amamvetsa chilichonse.+
15 Mtsogoleri woipa wolamulira anthu onyozeka ali ngati mkango wobangula ndiponso chimbalangondo chimene chikubwera kudzakuluma.+