Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zikakatero, inu mukavumbuluke ndi kukalanda mzindawo, pakuti Yehova Mulungu wanu adzaupereka ndithu m’manja mwanu.+

  • Oweruza 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Ndidzapulumutsa anthu inu pogwiritsa ntchito amuna 300 amene anamwa madzi ndi manja awo, ndipo ndidzapereka Amidiyani m’manja mwanu.+ Koma ena onsewa, aliyense abwerere kwawo.”

  • 1 Samueli 14:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho Yonatani anauza mtumiki wake womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa amuna osadulidwawa.+ Pakuti mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa anthu ake pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+

  • 2 Samueli 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno Davide anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, ndipereka ndithu Afilisitiwa m’manja mwako.”+

  • 2 Mafumu 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Zimenezi ndi zinthu zazing’ono kwambiri pamaso pa Yehova,+ ndipo ndithu apereka Amowabu m’manja mwanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena