Yeremiya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 kenako n’kubwera kudzaima pamaso panga m’nyumba iyi, imene yatchedwa ndi dzina langa+ n’kumanena kuti, ‘Ndithudi tidzapulumutsidwa,’ ngakhale mukuchita zinthu zonyansa zonsezi? Ezekieli 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ansembe ako aphwanya chilamulo changa modzionetsera,+ ndipo akuipitsa malo anga oyera.+ Sakusiyanitsa+ zinthu zoyera ndi zinthu wamba.+ Sanauze anthu kusiyana kwa zinthu zodetsedwa ndi zinthu zoyera.+ Anyalanyaza sabata langa+ ndipo andichitira mwano pakati pawo.+
10 kenako n’kubwera kudzaima pamaso panga m’nyumba iyi, imene yatchedwa ndi dzina langa+ n’kumanena kuti, ‘Ndithudi tidzapulumutsidwa,’ ngakhale mukuchita zinthu zonyansa zonsezi?
26 Ansembe ako aphwanya chilamulo changa modzionetsera,+ ndipo akuipitsa malo anga oyera.+ Sakusiyanitsa+ zinthu zoyera ndi zinthu wamba.+ Sanauze anthu kusiyana kwa zinthu zodetsedwa ndi zinthu zoyera.+ Anyalanyaza sabata langa+ ndipo andichitira mwano pakati pawo.+