Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Anamanga maguwa ansembe m’nyumba ya Yehova,+ imene ponena za iyo Yehova anati: “Ku Yerusalemu ndidzaikako dzina langa.”+

  • 2 Mbiri 33:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komanso iye anaika m’nyumba ya Mulungu woona+ chifaniziro+ chimene anapanga. Koma ponena za nyumba imeneyo, Mulungu anauza Davide ndi Solomo mwana wake kuti: “M’nyumba iyi ndiponso mu Yerusalemu mzinda umene ndausankha+ pa mafuko onse a Isiraeli, ndidzaikamo dzina langa+ mpaka kalekale.+

  • Yeremiya 34:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma inu munatembenuka ndi kuchita zolungama pamaso panga mwa kulengeza ufulu, aliyense kwa mnzake. Munachita pangano pamaso panga,+ m’nyumba imene ikutchedwa ndi dzina langa.+

  • Ezekieli 20:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 “Inu a nyumba ya Isiraeli, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pitani, aliyense wa inu akatumikire mafano ake onyansawo.+ Pambuyo pake, ngati simundimvera ndidzakusiyani ndipo simudzadetsanso dzina langa loyera ndi mphatso zanu ndiponso mafano anu onyansa.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena