Miyambo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngati munthu wodana nawe ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse madzi akumwa,+ Aroma 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musabwezere choipa pa choipa.+ Chitani zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino.
21 Ngati munthu wodana nawe ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse madzi akumwa,+