31 Munthu ameneyo wanyoza mawu a Yehova,+ ndipo waphwanya malamulo ake.+ Aziphedwa ndithu mosalephera.+ Mlandu wa cholakwa chake uzikhala ndi iye mwini.’”+
14 N’chifukwa chake ndalumbirira a m’nyumba ya Eli kuti mpaka kalekale sadzapewa chilango chifukwa cha cholakwa cha anthu a m’nyumba yakewo, ngakhale atapereka nsembe.”+
17 chifukwa chakuti andisiya n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho mkwiyo wanga wayakira malo ano ndipo suzimitsidwa.’”’+