1 Samueli 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndipo Yehova anakomera mtima Hana,+ moti anayamba kutenga pakati ndipo anabereka ana aamuna atatu ndi aakazi awiri.+ Mwanayo Samueli anapitiriza kukula, akukondedwa ndi Yehova.+ Miyambo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukachita zimenezi, Mulungu ndi anthu adzakukomera mtima ndipo adzakuona kuti ndiwe wozindikira.+ Luka 2:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Koma Yesu anali kukulabe m’nzeru+ ndi mu msinkhu. Ndipo Mulungu ndi anthu anapitiriza kukondwera naye.+
21 ndipo Yehova anakomera mtima Hana,+ moti anayamba kutenga pakati ndipo anabereka ana aamuna atatu ndi aakazi awiri.+ Mwanayo Samueli anapitiriza kukula, akukondedwa ndi Yehova.+
52 Koma Yesu anali kukulabe m’nzeru+ ndi mu msinkhu. Ndipo Mulungu ndi anthu anapitiriza kukondwera naye.+