Genesis 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano Yehova anakumbukira Sara monga mwa mawu ake, ndipo Yehovayo anachitira Sara monga momwe ananenera.+ Deuteronomo 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mudzakhala odalitsika mwa anthu onse.+ Pakati panu sipadzapezeka mwamuna, mkazi kapena chiweto chosabereka.+ 1 Samueli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anadzuka m’mawa kwambiri n’kugwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi pamaso pa Yehova. Atatero anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona+ ndi mkazi wake Hana, ndipo Yehova anayamba kum’kumbukira.+
21 Tsopano Yehova anakumbukira Sara monga mwa mawu ake, ndipo Yehovayo anachitira Sara monga momwe ananenera.+
14 Inu mudzakhala odalitsika mwa anthu onse.+ Pakati panu sipadzapezeka mwamuna, mkazi kapena chiweto chosabereka.+
19 Kenako anadzuka m’mawa kwambiri n’kugwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi pamaso pa Yehova. Atatero anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona+ ndi mkazi wake Hana, ndipo Yehova anayamba kum’kumbukira.+