1 Samueli 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukaonetsetse ndi kutsimikizira za malo onse obisika kumene iye amabisala. Kenako mudzabwerenso kwa ine ndi umboni, ndipo ine ndidzapita nanu. Ngati alidi m’dzikolo, ndidzam’funafuna mosamala pakati pa anthu masauzande+ ambirimbiriwo a Yuda.” 1 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine,+ pakuti iwe wandichitira zabwino,+ koma ine ndakuchitira zoipa.
23 Mukaonetsetse ndi kutsimikizira za malo onse obisika kumene iye amabisala. Kenako mudzabwerenso kwa ine ndi umboni, ndipo ine ndidzapita nanu. Ngati alidi m’dzikolo, ndidzam’funafuna mosamala pakati pa anthu masauzande+ ambirimbiriwo a Yuda.”
17 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine,+ pakuti iwe wandichitira zabwino,+ koma ine ndakuchitira zoipa.