1 Samueli 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Sauli anatenga amuna osankhidwa mwapadera 3,000+ mu Isiraeli monse, ndipo anapita kukafunafuna Davide+ ndi amuna amene anali kuyenda naye m’matanthwe amene mumakhala mbuzi za m’mapiri.+
2 Pamenepo Sauli anatenga amuna osankhidwa mwapadera 3,000+ mu Isiraeli monse, ndipo anapita kukafunafuna Davide+ ndi amuna amene anali kuyenda naye m’matanthwe amene mumakhala mbuzi za m’mapiri.+