Salimo 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Woipa amalondalonda munthu wolungama,+Ndipo amafuna kuti amuphe.+ Salimo 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu amene akufuna kundiwononga anditchera misampha,+Amene akufuna kundivulaza akulankhula motsutsana nane,+Ndipo amakhala akukonza zachinyengo tsiku lonse.+
12 Anthu amene akufuna kundiwononga anditchera misampha,+Amene akufuna kundivulaza akulankhula motsutsana nane,+Ndipo amakhala akukonza zachinyengo tsiku lonse.+