-
1 Samueli 28:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Sauli atamva zimenezi, anadzigwetsa mofulumira ndi kugona pansi mantha atamugwira kwambiri chifukwa cha mawu a “Samueli.” Komanso analefuka kwambiri chifukwa chakuti sanadye chakudya masana onse ndi usiku wonse.
-