1 Samueli 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho ananena kuti: “Ulemerero wachoka mu Isiraeli kupita kudziko lina,+ chifukwa likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+ Salimo 78:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Analola kuti chizindikiro cha mphamvu zake chitengedwe ndi adani ake,+Iye analola kuti chizindikiro cha kukongola kwake chikhale m’manja mwa adani.+
22 Choncho ananena kuti: “Ulemerero wachoka mu Isiraeli kupita kudziko lina,+ chifukwa likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+
61 Analola kuti chizindikiro cha mphamvu zake chitengedwe ndi adani ake,+Iye analola kuti chizindikiro cha kukongola kwake chikhale m’manja mwa adani.+