1 Samueli 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Davide sanasiye mwamuna ndi mkazi aliyense ali wamoyo kuti abwere nawo ku Gati, chifukwa ananena kuti: “Angakatinenere kuti, ‘Davide watichita zakutizakuti.’”+ (Izi n’zimene iye anali kuchita masiku onse amene anakhala kumidzi ya Afilisiti.)
11 Davide sanasiye mwamuna ndi mkazi aliyense ali wamoyo kuti abwere nawo ku Gati, chifukwa ananena kuti: “Angakatinenere kuti, ‘Davide watichita zakutizakuti.’”+ (Izi n’zimene iye anali kuchita masiku onse amene anakhala kumidzi ya Afilisiti.)