4 Kenako Sauli anauza womunyamulira zida+ kuti: “Solola lupanga lako+ undibaye nalo, kuti amuna osadulidwawa+ asandipeze ndi kundizunza.”+ Koma womunyamulira zida uja sanafune+ kuchita zimenezo, chifukwa anali kuchita mantha kwambiri. Chotero Sauli anatenga lupanga lake n’kuligwera.+