Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.

  • Deuteronomo 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Usaphe munthu.*+

  • Yakobo 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti amene anati: “Usachite chigololo,”+ anatinso: “Usaphe munthu.”+ Tsopano ngati iwe sunachite chigololo koma wapha munthu, walakwira chilamulo.

  • 1 Yohane 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Aliyense amene amadana+ ndi m’bale wake ndi wopha munthu,+ ndipo mukudziwa kuti aliyense wopha munthu+ sadzalandira moyo wosatha.+

  • Chivumbulutso 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma amantha, opanda chikhulupiriro,+ odetsedwa amenenso amachita zinthu zonyansa,+ opha anthu,+ adama,+ ochita zamizimu, opembedza mafano,+ ndi onse abodza,+ gawo lawo lidzakhala m’nyanja yoyaka moto+ ndi sulufule.+ Nyanja imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena