-
1 Samueli 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Tsopano Eli anaitana Samueli, n’kunena kuti: “Samueli, mwana wanga!” Ndipo iye anayankha kuti: “Ine mbuyanga.”
-
-
1 Samueli 4:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Tsopano mwamuna uja anauza Eli kuti: “Ine ndikuchokera kumalo omenyera nkhondo, ndithudi ndachita kuthawa kumeneko lero.” Pamenepo Eli anam’funsa kuti: “Chachitika n’chiyani mwana wanga?”
-