Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kumene inu mudzafere inenso ndidzafera komweko,+ ndipo ndidzaikidwanso komweko. Yehova andilange kwambiri+ ngati chinachake kupatulapo imfa chingandilekanitse ndi inu.”

  • 1 Samueli 20:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova andilange ine Yonatani mowirikiza,+ ndikadziwa kuti bambo anga akufuna kukuchitira choipa koma osakudziwitsa ndi kukulola kuti uchoke, moti iweyo n’kulepheradi kuchoka mwamtendere. Yehova akhale nawe+ monga mmene anakhalira ndi bambo anga.+

  • 2 Samueli 19:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Amasa mumuuze kuti,+ ‘Kodi iwe sindiwe fupa langa ndi mnofu wanga? Mulungu andilange mowirikiza+ ngati sudzakhala mtsogoleri wa gulu langa lankhondo nthawi zonse m’malo mwa Yowabu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena