1 Samueli 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Likasa la pangano la Yehova litafika mumsasa, Aisiraeli onse anafuula mokweza kwambiri,+ moti kunali chisokonezo m’dziko lonse. 1 Samueli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngakhalenso likasa la Mulungu linalandidwa,+ ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anafa.+ Salimo 78:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Analola kuti chizindikiro cha mphamvu zake chitengedwe ndi adani ake,+Iye analola kuti chizindikiro cha kukongola kwake chikhale m’manja mwa adani.+
5 Likasa la pangano la Yehova litafika mumsasa, Aisiraeli onse anafuula mokweza kwambiri,+ moti kunali chisokonezo m’dziko lonse.
61 Analola kuti chizindikiro cha mphamvu zake chitengedwe ndi adani ake,+Iye analola kuti chizindikiro cha kukongola kwake chikhale m’manja mwa adani.+