1 Samueli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo m’nyumba yanga udzangoona mdani pakati pa zinthu zonse zabwino zimene zidzachitikira Isiraeli.+ M’nyumba yako simudzapezeka munthu wokalamba. 1 Samueli 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo chizindikiro chako chimene chidzachitikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinihasi+ ndi ichi: Onse awiri adzafa tsiku limodzi.+
32 Ndipo m’nyumba yanga udzangoona mdani pakati pa zinthu zonse zabwino zimene zidzachitikira Isiraeli.+ M’nyumba yako simudzapezeka munthu wokalamba.
34 Ndipo chizindikiro chako chimene chidzachitikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinihasi+ ndi ichi: Onse awiri adzafa tsiku limodzi.+