Deuteronomo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Dzanja+ la Yehova linali pa iwo kuwasautsa ndi kuwachotsa pakati panu, kufikira onse atatha.+ 1 Samueli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero Afilisiti anagonjetsedwa ndipo sanabwerenso m’dziko la Isiraeli.+ Dzanja la Yehova linapitiriza kukankhira kutali Afilisiti masiku onse a moyo wa Samueli.+
13 Chotero Afilisiti anagonjetsedwa ndipo sanabwerenso m’dziko la Isiraeli.+ Dzanja la Yehova linapitiriza kukankhira kutali Afilisiti masiku onse a moyo wa Samueli.+