1 Samueli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngakhalenso likasa la Mulungu linalandidwa,+ ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anafa.+ 1 Samueli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Afilisiti anatenga likasa+ la Mulungu woona kuchoka nalo ku Ebenezeri n’kupita nalo ku Asidodi.+ Salimo 78:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Analola kuti chizindikiro cha mphamvu zake chitengedwe ndi adani ake,+Iye analola kuti chizindikiro cha kukongola kwake chikhale m’manja mwa adani.+
5 Tsopano Afilisiti anatenga likasa+ la Mulungu woona kuchoka nalo ku Ebenezeri n’kupita nalo ku Asidodi.+
61 Analola kuti chizindikiro cha mphamvu zake chitengedwe ndi adani ake,+Iye analola kuti chizindikiro cha kukongola kwake chikhale m’manja mwa adani.+