Rute 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsiku lina Rute mkazi wachimowabu uja anapempha Naomi kuti: “Chonde ndiloleni ndipite kuminda ndikakunkhe+ balere m’mbuyo mwa aliyense amene angandikomere mtima.” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.” Rute 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Rute anapitiriza kukhala pafupi ndi atsikana antchito a Boazi, mpaka pamene anamaliza kukolola balere+ ndi tirigu. Ndipo anapitiriza kukhala ndi apongozi ake.+
2 Tsiku lina Rute mkazi wachimowabu uja anapempha Naomi kuti: “Chonde ndiloleni ndipite kuminda ndikakunkhe+ balere m’mbuyo mwa aliyense amene angandikomere mtima.” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.”
23 Choncho Rute anapitiriza kukhala pafupi ndi atsikana antchito a Boazi, mpaka pamene anamaliza kukolola balere+ ndi tirigu. Ndipo anapitiriza kukhala ndi apongozi ake.+