Salimo 56:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzadalira inu, tsiku lililonse limene ndingachite mantha.+ Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+