Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Zikatero, Yehova anali kuwapatsa oweruza,+ ndipo anali kuwapulumutsa m’manja mwa ofunkha.+

  • 1 Samueli 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ anadziwa kuti Samueli ndiye anali wovomerezeka kukhala mneneri wa Yehova.+

  • 1 Samueli 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+

  • 1 Samueli 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Patapita nthawi, Samueli+ anamwalira ndipo Aisiraeli onse anasonkhana pamodzi ndi kulira+ maliro ake. Iwo anamuika m’manda panyumba yake ku Rama.+ Kenako Davide ananyamuka ndi kupita kuchipululu cha Parana.+

  • Machitidwe 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Zonsezi zinachitika m’zaka pafupifupi 450.

      “Zimenezi zitatha anawapatsa oweruza mpaka kudzafika pa mneneri Samueli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena