Genesis 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Adamu anagona ndi Hava mkazi wake, ndipo mkaziyo anatenga pakati.+ M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anabereka Kaini*+ n’kunena kuti: “Ndabereka mwana wamwamuna ndi thandizo la Yehova.”+ Rute 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Boazi anatenga Rute kukhala mkazi wake ndipo anagona naye. Pamenepo Yehova anam’dalitsa ndipo anatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna.
4 Kenako Adamu anagona ndi Hava mkazi wake, ndipo mkaziyo anatenga pakati.+ M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anabereka Kaini*+ n’kunena kuti: “Ndabereka mwana wamwamuna ndi thandizo la Yehova.”+
13 Choncho Boazi anatenga Rute kukhala mkazi wake ndipo anagona naye. Pamenepo Yehova anam’dalitsa ndipo anatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna.