1 Samueli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.” 1 Samueli 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma anthuwo anakana kumvera mawu a Samueli+ ndipo anati: “Ife tikufuna kuti mfumu izitilamulira. 1 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano mfumu imene mwasankha ndi imeneyi, mfumu imene mwapempha.+ Ndipotu Yehova wakuikiranidi mfumu+ yoti izikulamulirani.
5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”
13 Tsopano mfumu imene mwasankha ndi imeneyi, mfumu imene mwapempha.+ Ndipotu Yehova wakuikiranidi mfumu+ yoti izikulamulirani.