1 Samueli 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Poyankha akulu a ku Yabesi anati: “Utipatse masiku 7 kuti titumize amithenga m’dziko lonse la Isiraeli, ndipo ngati sipapezeka wotipulumutsa,+ pamenepo tibwera kwa iwe.”
3 Poyankha akulu a ku Yabesi anati: “Utipatse masiku 7 kuti titumize amithenga m’dziko lonse la Isiraeli, ndipo ngati sipapezeka wotipulumutsa,+ pamenepo tibwera kwa iwe.”