Yoswa 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+ 1 Samueli 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Hana anaimirira atadya ndi kumwa ku Silo. Apa n’kuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi+ wa Yehova.
18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+
9 Pamenepo Hana anaimirira atadya ndi kumwa ku Silo. Apa n’kuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi+ wa Yehova.