1 Samueli 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atamaliza kudya ndi kumwa ku Silo, Hana anaimirira. Apa nʼkuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi*+ wa Yehova. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 15
9 Atamaliza kudya ndi kumwa ku Silo, Hana anaimirira. Apa nʼkuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi*+ wa Yehova.