Yoswa 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kefara-amoni, Ofini, ndi Geba.+ Mizinda 12 ndi midzi yake. 1 Samueli 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yonatani anakantha mudzi wa asilikali+ a Afilisiti+ umene unali ku Geba,+ ndipo Afilisiti anamva zimenezi. Zitatero Sauli analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ m’dziko lonse n’kunena kuti: “Imvani Aheberi inu!”
3 Kenako Yonatani anakantha mudzi wa asilikali+ a Afilisiti+ umene unali ku Geba,+ ndipo Afilisiti anamva zimenezi. Zitatero Sauli analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ m’dziko lonse n’kunena kuti: “Imvani Aheberi inu!”