Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Amuna 300+ aja anapitiriza kuliza malipenga,+ ndipo Yehova anachititsa Amidiyani kuukirana okhaokha mumsasa wonsewo.+ Anthu onse a mumsasawo anathawa mpaka kukafika ku Beti-sita, ndi ku Zerera mpaka kumalire kwa mzinda wa Abele-mehola+ pafupi ndi Tabati.

  • 2 Mbiri 20:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ana a Amoni ndi ana a Mowabu anaukira anthu okhala kudera lamapiri la Seiri+ ndipo anawapha ndi kuwamaliza. Atatha kupha anthu a ku Seiri, iwo anaphana okhaokha.+

  • Yesaya 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Ndidzachititsa kuti Aiguputo ayambane ndi Aiguputo anzawo. Aliyense adzamenyana ndi m’bale wake ndipo aliyense adzamenyana ndi mnzake. Mzinda udzamenyana ndi mzinda unzake ndipo ufumu udzamenyana ndi ufumu unzake.+

  • Ezekieli 38:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘Ndidzamubweretsera lupanga m’madera anga onse a m’mapiri kuti limuwononge,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Aliyense adzapha m’bale wake ndi lupanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena