1 Samueli 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthuwo atalowa m’nkhalangomo, anaona uchi+ ukukha. Pa nthawiyi panalibe amene anadya, chifukwa anali kuopa lumbiro lija.+ Machitidwe 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndipo atadya chakudya anapezanso mphamvu.+ Kwa masiku angapo anakhala ndi ophunzira ku Damasiko.+
26 Anthuwo atalowa m’nkhalangomo, anaona uchi+ ukukha. Pa nthawiyi panalibe amene anadya, chifukwa anali kuopa lumbiro lija.+