Deuteronomo 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ungokhala wotsimikiza mtima kwambiri kusadya magazi,+ chifukwa magazi ndiwo moyo,+ ndipo suyenera kudya nyama pamodzi ndi moyo wake. Deuteronomo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma magazi ake okha usadye.+ Uziwathira pansi ngati madzi.+
23 Koma ungokhala wotsimikiza mtima kwambiri kusadya magazi,+ chifukwa magazi ndiwo moyo,+ ndipo suyenera kudya nyama pamodzi ndi moyo wake.