Genesis 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma musadye+ nyama pamodzi ndi magazi+ ake, amene ndiwo moyo+ wake. Levitiko 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Musamadye magazi+ alionse kulikonse kumene mungakhale, kaya akhale magazi a mbalame kapena a nyama. Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake. 1 Samueli 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano anthu anauza Sauli kuti: “Taonani! Anthu akuchimwira Yehova mwa kudya nyama pamodzi ndi magazi ake.”+ Chotero iye anati: “Mwachita zinthu mosakhulupirika. Choyamba, kunkhunizani chimwala mubwere nacho kuno.” Machitidwe 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ dama,*+ zopotola,+ ndi magazi.+
26 “‘Musamadye magazi+ alionse kulikonse kumene mungakhale, kaya akhale magazi a mbalame kapena a nyama.
10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
33 Tsopano anthu anauza Sauli kuti: “Taonani! Anthu akuchimwira Yehova mwa kudya nyama pamodzi ndi magazi ake.”+ Chotero iye anati: “Mwachita zinthu mosakhulupirika. Choyamba, kunkhunizani chimwala mubwere nacho kuno.”
20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ dama,*+ zopotola,+ ndi magazi.+