Salimo 94:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo amalankhula zopanda pake, ndipo amalankhula mosasamala.+Onse ochita zopweteka anzawo amadzitukumula.+ Yakobo 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati munthu akudziona ngati wopembedza,+ koma salamulira lilime lake,+ ndipo akupitiriza kunyenga mtima wake,+ kupembedza kwa munthu ameneyu n’kopanda pake.+ Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+
4 Iwo amalankhula zopanda pake, ndipo amalankhula mosasamala.+Onse ochita zopweteka anzawo amadzitukumula.+
26 Ngati munthu akudziona ngati wopembedza,+ koma salamulira lilime lake,+ ndipo akupitiriza kunyenga mtima wake,+ kupembedza kwa munthu ameneyu n’kopanda pake.+
8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+