Genesis 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwamunayo anayankha kuti: “Mkazi amene munandipatsayu ndi amene wandipatsa chipatso cha mtengowo, ndipo ine ndadya.”+ Ekisodo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo Aroni anayankha kuti: “Mkwiyo wa mbuyanga usayake. Inuyo mukuwadziwa bwino anthuwa, kuti amakonda kuchita zoipa.+ 1 Samueli 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthuwa+ atenga pa zofunkha, nkhosa ndi ng’ombe zabwino kwambiri, pa zinthu zimene zinayenera kuwonongedwa, kuti azipereke nsembe+ kwa Yehova Mulungu wanu ku Giligala.”+
12 Mwamunayo anayankha kuti: “Mkazi amene munandipatsayu ndi amene wandipatsa chipatso cha mtengowo, ndipo ine ndadya.”+
22 Ndipo Aroni anayankha kuti: “Mkwiyo wa mbuyanga usayake. Inuyo mukuwadziwa bwino anthuwa, kuti amakonda kuchita zoipa.+
21 Anthuwa+ atenga pa zofunkha, nkhosa ndi ng’ombe zabwino kwambiri, pa zinthu zimene zinayenera kuwonongedwa, kuti azipereke nsembe+ kwa Yehova Mulungu wanu ku Giligala.”+